Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili M‘buku la Zefaniya ZEFANIYA ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Tsiku la chiweruzo la Yehova lili pafupi (1-18) Tsiku la Yehova likubwera mofulumira (14) Siliva ndi golide sizingapulumutse munthu (18) 2 Funafunani Yehova tsiku la mkwiyo wake lisanafike (1-3) Yesetsani kukhala olungama ndi ofatsa (3) “Mwina mungadzabisike” (3) Kuweruza mitundu yozungulira (4-15) 3 Yerusalemu, mzinda wogalukira ndiponso wachinyengo (1-7) Kuweruza ndiponso kubwezeretsa (8-20) Kusintha nʼkuyamba kulankhula chilankhulo choyera (9) Anthu odzichepetsa komanso ooneka onyozeka adzapulumutsidwa (12) Yehova adzakondwera ndi Ziyoni (17)