MALIKO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Yohane Mʼbatizi ankalalikira (1-8)
Kubatizidwa kwa Yesu (9-11)
Yesu anayesedwa ndi Satana (12, 13)
Yesu anayamba kulalikira ku Galileya (14, 15)
Anasankha ophunzira oyambirira (16-20)
Anatulutsa mzimu wonyansa (21-28)
Yesu anachiritsa anthu ambiri ku Kaperenao (29-34)
Anapemphera kumalo opanda anthu (35-39)
Munthu wakhate anachiritsidwa (40-45)
-
Yesu anasintha maonekedwe ake (1-13)
Mnyamata wogwidwa ndi chiwanda anachiritsidwa (14-29)
Zinthu zonse ndi zotheka kwa munthu amene ali ndi chikhulupiriro (23)
Yesu ananeneratu kachiwiri za imfa yake (30-32)
Ophunzira anakangana kuti wamkulu ndi ndani (33-37)
Aliyense amene sakulimbana nafe ali kumbali yathu (38-41)
Zopunthwitsa (42-48)
“Khalani ndi mchere mwa inu nokha” (49, 50)
-
Ukwati komanso kutha kwa banja (1-12)
Yesu anadalitsa ana (13-16)
Funso la munthu wachuma (17-25)
Zinthu zimene tikuyenera kudzimana chifukwa cha Ufumu (26-31)
Yesu ananeneratunso za imfa yake (32-34)
Pempho la Yakobo ndi Yohane (35-45)
Yesu anapereka dipo kuti awombole anthu ambiri (45)
Batimeyu amene anali ndi vuto losaona anachiritsidwa (46-52)
-
Ansembe anakonza zoti aphe Yesu (1, 2)
Anathira Yesu mafuta onunkhira kwambiri (3-9)
Yudasi anapereka Yesu (10, 11)
Pasika womaliza (12-21)
Anayambitsa Mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (22-26)
Ananeneratu zoti Petulo adzamukana (27-31)
Yesu anapemphera ku Getsemane (32-42)
Yesu anagwidwa (43-52)
Anaimbidwa mlandu Mʼkhoti Lalikulu la Ayuda (53-65)
Petulo anakana Yesu (66-72)
-
Yesu anaukitsidwa (1-8)