Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la Aefeso AEFESO ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1, 2) Madalitso auzimu (3-7) Kusonkhanitsa zinthu zonse kwa Akhristu (8-14) Kukhazikitsa “dongosolo” pa nthawi imene anaikiratu (10) Anaikidwa chidindo ndi mzimu woyera ngati “chikole chotsimikizira” (13, 14) Paulo anathokoza Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro cha Aefeso ndipo anawapempherera (15-23) 2 Anapangitsa kuti akhale amoyo mogwirizana ndi Khristu (1-10) Anagwetsa khoma lomwe linkawalekanitsa (11-22) 3 Chinsinsi chopatulika chinaphatikizapo anthu a mitundu ina (1-13) Anthu a mitundu ina adzalamulira limodzi ndi Khristu (6) Cholinga chamuyaya cha Mulungu (11) Anapempherera Aefeso kuti akhale ozindikira (14-21) 4 Ogwirizana mʼthupi la Khristu (1-16) Mphatso za amuna (8) Umunthu wakale komanso watsopano (17-32) 5 Malankhulidwe komanso khalidwe loyera (1-5) Muziyenda ngati ana a kuwala (6-14) Mudzazidwe ndi mzimu (15-20) Muzigwiritsa ntchito bwino nthawi yanu (16) Malangizo opita kwa amuna ndi akazi apabanja (21-33) 6 Malangizo opita kwa makolo ndi ana (1-4) Malangizo opita kwa akapolo ndi ambuye (5-9) Zida zonse zankhondo zochokera kwa Mulungu (10-20) Moni womaliza (21-24)