Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la Akolose AKOLOSE ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1, 2) Kuthokoza chifukwa cha chikhulupiriro cha Akolose (3-8) Kuwapempherera kuti akule mwauzimu (9-12) Udindo waukulu wa Khristu (13-23) Paulo anagwira ntchito mwakhama pothandiza mpingo (24-29) 2 Chinsinsi chopatulika cha Mulungu, Khristu (1-5) Samalani ndi anthu opusitsa anzawo (6-15) Zenizeni zake zinakwaniritsidwa ndi Khristu (16-23) 3 Umunthu wakale komanso watsopano (1-17) Chititsani ziwalo za thupi lanu kukhala zakufa (5) Chikondi chimagwirizanitsa anthu mwamphamvu kwambiri kuposa chinthu china chilichonse (14) Malangizo opita ku mabanja a Chikhristu (18-25) 4 Malangizo opita kwa ambuye (1) “Muzilimbikira kupemphera” (2-4) Kuchita zinthu mwanzeru pokhala ndi anthu akunja (5, 6) Moni womaliza (7-18)