Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Zimene Zili Mʼbuku la 1 Atesalonika

1 ATESALONIKA

ZIMENE ZILI MʼBUKULI

  • 1

    • Moni (1)

    • Kuthokoza chifukwa cha chikhulupiriro cha Atesalonika (2-10)

  • 2

    • Utumiki wa Paulo ku Tesalonika (1-12)

    • Atesalonika analandira mawu a Mulungu (13-16)

    • Paulo ankalakalaka kuona Atesalonika (17-20)

  • 3

    • Paulo anapitiriza kukhala ku Atene podikira lipoti lochokera ku Tesalonika (1-5)

    • Timoteyo anabweretsa lipoti lolimbikitsa (6-10)

    • Anapempherera Atesalonika (11-13)

  • 4

    • Anawachenjeza kuti azipewa chiwerewere (1-8)

    • Muzikondana kwambiri kuposa mmene mukuchitira (9-12)

      • “Musamalowerere nkhani za ena” (11)

    • Amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambirira kuuka (13-18)

  • 5

    • Kubwera kwa tsiku la Yehova (1-5)

      • “Bata ndi mtendere!” (3)

    • Khalanibe maso komanso oganiza bwino (6-11)

    • Kuwalimbikitsa (12-24)

    • Moni womaliza (25-28)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena