Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la 2 Atesalonika 2 ATESALONIKA ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1, 2) Chikhulupiriro cha Atesalonika chinkakulirakulira (3-5) Anthu osamvera adzalandira chilango (6-10) Ankapempherera mpingo (11, 12) 2 Munthu wosamvera malamulo (1-12) Anawalimbikitsa kuti akhale olimba (13-17) 3 Pitirizani kupemphera (1-5) Anawachenjeza kuti apewe makhalidwe osalongosoka (6-15) Moni womaliza (16-18)