Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la 1 Timoteyo 1 TIMOTEYO ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1, 2) Chenjezo lokhudza aphunzitsi abodza (3-11) Paulo anasonyezedwa kukoma mtima kwakukulu (12-16) Mfumu yamuyaya (17) “Kumenya nkhondo yabwino” (18-20) 2 Kupempherera anthu osiyanasiyana (1-7) Mulungu mmodzi, mkhalapakati mmodzi (5) Dipo lokwanira ndendende (6) Malangizo kwa amuna ndi akazi (8-15) Kuvala mwaulemu (9, 10) 3 Zoyenera kuti munthu akhale woyangʼanira (1-7) Zoyenera kuti munthu akhale mtumiki wothandiza (8-13) Chinsinsi chopatulika cha kudzipereka kwa Mulungu (14-16) 4 Chenjezo lokhudza zomwe ziwanda zimaphunzitsa (1-5) Kukhala mtumiki wabwino wa Khristu (6-10) Kulimbitsa thupi ndiponso kudzipereka kwa Mulungu (8) Uzisamala ndi zimene umaphunzitsa (11-16) 5 Zoyenera kuchita ndi achikulire komanso achinyamata (1, 2) Kuthandiza akazi amasiye (3-16) Kusamalira banja (8) Kulemekeza akulu akhama (17-25) ‘Vinyo pangʼono, chifukwa cha vuto la mʼmimba’ (23) 6 Akapolo azilemekeza ambuye awo (1, 2) Aphunzitsi onyenga ndiponso kukonda ndalama (3-10) Malangizo kwa munthu wa Mulungu (11-16) Kulemera pa ntchito zabwino (17-19) Sunga zimene unalandira (20, 21)