Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la 2 Timoteyo 2 TIMOTEYO ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1, 2) Paulo anayamikira Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro cha Timoteyo (3-5) Kukolezera moto mphatso yochokera kwa Mulungu (6-11) Gwiritsitsabe mawu olondola (12-14) Adani ndi anzake a Paulo (15-18) 2 Kuphunzitsa oyenerera kukhala aphunzitsi (1-7) Kuvutika chifukwa cha uthenga wabwino (8-13) Kufotokoza bwino mawu a choonadi (14-19) Kuthawa zilakolako za unyamata (20-22) Zoyenera kuchita ndi otsutsa (23-26) 3 Masiku otsiriza adzakhala nthawi yovuta (1-7) Kutsatira chitsanzo cha Paulo (8-13) “Pitiriza kutsatira zimene unaphunzira” (14-17) Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu (16) 4 “Uzikwaniritsa mbali zonse za utumiki wako” (1-5) Lalikira mawu modzipereka (2) “Ndamenya nkhondo yabwino” (6-8) Zina zomwe Paulo ananena (9-18) Kupereka moni (19-22)