Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la Tito TITO ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1-4) Tito aike akulu ku Kerete (5-9) Kudzudzula anthu osalamulirika (10-16) 2 Malangizo abwino kwa achinyamata ndi achikulire (1-15) Kukana moyo wosaopa Mulungu (12) Kudzipereka pa ntchito zabwino (14) 3 Kugonjera koyenera (1-3) Kukonzekera ntchito zabwino (4-8) Kupewa mpatuko komanso kutsutsana pa zinthu zopusa (9-11) Malangizo ena komanso moni (12-15)