YOSWA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Aisiraeli anawoloka Yorodano (1-17)
-
Miyala ya chikumbutso (1-24)
-
Mizinda yothawirako (1-9)
-
Yoswa anafotokoza mbiri ya Aisiraeli (1-13)
Anawalimbikitsa kutumikira Yehova (14-24)
“Ine ndi banja langa tizitumikira Yehova” (15)
Yoswa anachita pangano ndi Aisiraeli (25-28)
Yoswa anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda (29-31)
Mafupa a Yosefe anaikidwa mʼmanda ku Sekemu (32)
Eliezara anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda (33)