Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili mu 2 Yohane 2 YOHANE ZIMENE ZILI MʼBUKULI Moni (1-3) Pitirizani kuyenda mʼchoonadi (4-6) Samalani ndi anthu opusitsa anzawo (7-11) Musamupatse moni (10, 11) Kukonza zoti akawachezere; kuwapatsa moni (12, 13)