Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la Yuda YUDA ZIMENE ZILI MʼBUKULI Moni (1, 2) Aphunzitsi abodza adzaweruzidwa (3-16) Mikayeli anakangana ndi Mdyerekezi (9) Ulosi wa Inoki (14, 15) Mupitirize kuchita zinthu zimene zingachititse kuti Mulungu azikukondani (17-23) Mulungu ndi woyenera ulemerero (24, 25)