CHIVUMBULUTSO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Mwanawankhosa anamatula zidindo 6 zoyambirira (1-17)
Wogonjetsa adani anakwera pahatchi yoyera (1, 2)
Amene anakwera pahatchi yofiira ngati moto analoledwa kuchotsa mtendere (3, 4)
Amene anakwera pahatchi yakuda anabweretsa njala (5, 6)
Amene anakwera pahatchi yotuwa dzina lake ndi Imfa (7, 8)
Pansi pa guwa lansembe panali anthu amene anaphedwa (9-11)
Chivomerezi chachikulu (12-17)