Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la Rute RUTE ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Banja la Elimeleki linasamukira ku Mowabu (1, 2) Naomi, Olipa ndi Rute anakhala amasiye (3-6) Rute anakhala wokhulupirika kwa Naomi ndi Mulungu wake (7-17) Naomi anabwerera ku Betelehemu ndi Rute (18-22) 2 Rute anakakunkha mʼmunda wa Boazi (1-3) Rute anakumana ndi Boazi (4-16) Rute anauza Naomi kuti Boazi anamukomera mtima (17-23) 3 Naomi anapereka malangizo kwa Rute (1-4) Rute ndi Boazi kopunthira mbewu (5-15) Rute anabwerera kwa Naomi (16-18) 4 Boazi anakhala wowombola (1-12) Boazi ndi Rute anabereka Obedi (13-17) Mzere wa makolo a Davide (18-22)