Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Talimasulira kuchokera ku Baibulo lachingelezi la New World Translation of the Holy Scriptures—lokonzedwanso mu 1984—
“Yehova, [יהוה, YHWH] Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘ . . . Ndikulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano. Zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso ndipo sizidzabweranso mumtima.’”—Yesaya 65:13, 17; onaninso 2 Petulo 3:13.
© 2010
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY
OF PENNSYLVANIA
100 Watchtower Drive
Patterson, NY 12563-9204 U.S.A.
OFALITSA
WATCHTOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY
OF NEW YORK, INC.
Brooklyn, New York, U.S.A.
Baibuloli lafalitsidwa lathunthu kapena mbali chabe m’zinenero zoposa 120. Kuti mudziwe zinenerozi, onani webusaiti ya www.pr2711.com/ny.
Mabaibulo onse a Dziko Latsopano amene asindikizidwa m’zinenero zonsezi alipo: 208,366,928
Lasindikizidwa mu February 2015
Baibuloli sitigulitsa. Mboni za Yehova zimalipereka pa ntchito yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse.
Timalipereka pa ntchito yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse, ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chichewa (bi12-CN)
Made in Japan
Lopangidwa ku Japan
4-7-1 Nakashinden
Ebina City
Kanagawa-Pref
243-0496
Japan