YEREMIYA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Yeremiya anasankhidwa kuti akhale mneneri (1-10)
Masomphenya a mtengo wa amondi (11, 12)
Masomphenya a mphika (13-16)
Yeremiya analimbikitsidwa kuti agwire ntchito yake (17-19)
2
3
Isiraeli anapanduka kwambiri (1-5)
Isiraeli ndi Yuda anachita tchimo la chigololo (6-11)
Anawalimbikitsa kuti alape (12-25)
4
Kulapa kumabweretsa madalitso (1-4)
Tsoka lidzachokera kumpoto (5-18)
Yeremiya anamva kupweteka mumtima chifukwa cha tsoka limene linkabwera (19-31)
5
Anthu anakana malangizo a Yehova (1-13)
Adzawonongedwa koma sadzawawononga onse (14-19)
Yehova anaimba mlandu anthu (20-31)
6
Nthawi yoti Yerusalemu azunguliridwe yayandikira (1-9)
Yehova anakwiyira Yerusalemu (10-21)
Anaukiridwa mwankhanza ndi anthu akumpoto (22-26)
Yeremiya anasandutsidwa woyenga zitsulo (27-30)
7
Kukhulupirira kachisi wa Yehova sikunawathandize (1-11)
Kachisi adzakhala ngati Silo (12-15)
Mulungu sasangalala ndi kulambira kwachinyengo (16-34)
8
Anthu anasankha njira imene anthu ambiri ankaitsatira (1-7)
Kodi anthu angakhale ndi nzeru popanda mawu a Yehova? (8-17)
Yeremiya analira chifukwa cha kuwonongedwa kwa Yuda (18-22)
9
Yeremiya anali ndi chisoni chachikulu (1-3a)
Yehova anaimba mlandu Yuda (3b-16)
Kulirira Yuda (17-22)
Adzitame chifukwa chodziwa Yehova (23-26)
10
Milungu ya anthu a mitundu ina singafanane ndi Mulungu wamoyo (1-16)
Nthawi yoti awonongedwe komanso kutengedwa kupita kudziko lina yayandikira (17, 18)
Yeremiya anamva chisoni (19-22)
Pemphero la mneneri (23-25)
11
Yuda anaphwanya pangano limene anapanga ndi Mulungu (1-17)
Yeremiya anali ngati mwana wa nkhosa amene akupita kukaphedwa (18-20)
Yeremiya anatsutsidwa ndi anthu akwawo (21-23)
12
13
Lamba wa nsalu amene anawonongeka (1-11)
Mitsuko ya vinyo idzaphwanyidwa (12-14)
Yuda amene sangathenso kusintha adzatengedwa kupita ku ukapolo (15-27)
14
Chilala, njala ndi lupanga (1-12)
Aneneri abodza adzawonongedwa (13-18)
Yeremiya anavomereza kuti anthuwo anali ochimwa (19-22)
15
Yehova sadzasintha chiweruzo chake (1-9)
Kudandaula kwa Yeremiya (10)
Zimene Yehova anayankha (11-14)
Pemphero la Yeremiya (15-18)
Yeremiya analimbikitsidwa ndi Yehova (19-21)
16
Yeremiya anauzidwa kuti asakwatire, kulira kapena kusala kudya (1-9)
Anapatsidwa chilango kenako nʼkubwezeretsedwa mwakale (10-21)
17
Tchimo la Yuda lalembedwa mochita kugoba (1-4)
Madalitso amene amabwera chifukwa chokhulupirira Yehova (5-8)
Mtima ndi wopusitsa (9-11)
Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli (12, 13)
Pemphero la Yeremiya (14-18)
Sabata lizikhala lopatulika (19-27)
18
Dongo mʼdzanja la wowumba (1-12)
Yehova adzafulatira Isiraeli (13-17)
Chiwembu chimene anakonzera Yeremiya komanso kuchonderera kwake (18-23)
19
20
Pasuri anamenya Yeremiya (1-6)
Yeremiya sangasiye kulalikira (7-13)
Kudandaula kwa Yeremiya (14-18)
21
22
23
Abusa abwino komanso oipa (1-4)
Tidzakhala otetezeka mu ulamuliro wa “mfumu yolungama” (5-8)
Aneneri abodza anadzudzulidwa (9-32)
“Katundu wolemera” wa Yehova (33-40)
24
25
26
27
28
29
30
31
32
Yeremiya anagula munda (1-15)
Pemphero la Yeremiya (16-25)
Zimene Yehova anayankha (26-44)
33
Analonjezedwa kuti adzabwerera mwakale (1-13)
Tidzakhala otetezeka mu ulamuliro wa “mfumu yolungama” (14-16)
Pangano limene anachita ndi Davide komanso ansembe (17-26)
34
35
36
Yeremiya ankanena mawu oti alembedwe mumpukutu (1-7)
Baruki anawerenga mpukutu mokweza (8-19)
Yehoyakimu anawotcha mpukutu (20-26)
Uthengawo unalembedwanso mumpukutu watsopano (27-32)
37
Akasidi anabwerera kwa kanthawi kochepa (1-10)
Yeremiya anaikidwa mʼndende (11-16)
Zedekiya anakumana ndi Yeremiya (17-21)
38
Yeremiya anaponyedwa mʼchitsime (1-6)
Ebedi-meleki anapulumutsa Yeremiya (7-13)
Yeremiya analimbikitsa Zedekiya kuti adzipereke mʼmanja mwa Ababulo (14-28)
39
Kuwonongedwa kwa Yerusalemu (1-10)
Yeremiya ankayenera kulonderedwa (11-14)
Ebedi-meleki anapulumutsidwa (15-18)
40
Nebuzaradani anamasula Yeremiya (1-6)
Gedaliya anasankhidwa kuti akhale wolamulira dziko (7-12)
Chiwembu chimene anakonzera Gedaliya (13-16)
41
42
43
44
45
46
47
48
49
Ulosi wokhudza Aamoni (1-6)
Ulosi wokhudza Edomu (7-22)
Ulosi wokhudza Damasiko (23-27)
Ulosi wokhudza Kedara ndi Hazori (28-33)
Ulosi wokhudza Elamu (34-39)
50
51
52
Zedekiya anagalukira mfumu ya Babulo (1-3)
Nebukadinezara anazungulira Yerusalemu (4-11)
Kuwonongedwa kwa mzinda komanso kachisi (12-23)
Anthu anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo (24-30)
Yehoyakini anatulutsidwa mʼndende (31-34)