Tsamba 2
Ndi za mtengo wapatali chotani nanga nzeru zathu zonse zambiri zodziŵira zinthu zimene zimatilola kusangalala ndi moyo! Chikhalirechobe ambiri aife timatenga zimenezi mosasamala. Kodi ndi thandizo lotani limene liripo kwa anthu ovulazika nzeru zodziŵira zinthu? Ngakhale kuti luso lazopangapanga lamakono lapereka thandizo, phunzirani ponena za yankho lokhutiritsadi ku vuto limeneli.