Tsamba 2
Kwa nthaŵi yaitali madinosaur asangalatsa ponse paŵiri achichepere ndi achikulire.
Kodi nyamazi zinali chiyani?
Kodi zinakhalako liti?
Kodi nchifukwa ninji zinazimiririka pa dziko lapansi?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Dinamation International