Zamkatimu
April 8, 2001
Kodi N’chifukwa Chiyani Mizinda Ili M’mavuto?
Anthu akudzazana kwambiri m’mizinda. Komano, mizinda ikuluikulu yagwa m’mavuto chifukwa cholephera kuwakwanitsa.
3 “Kusefukira Kwa Anthu M’mizinda”
4 Kodi N’Chifukwa Chiyani Mizinda Ili M’mavuto?
8 Kodi Tsogolo la Mizinda Ndi Lotani?
11 Mmene Nkhondo Zamasiku Ano Zilili
12 Zida Zazing’ono Koma Mavuto Aakulu
17 Kodi Zoletsa Zida Zitha Bwanji M’tsogolo Muno?
25 Kuyang’anitsitsa Tsitsi Lanu
28 Kusintha Dera Louma Kukhala Lachonde
32 Anthu Ambiri Adzapita—Nanga Inu Bwanji?
Kulimbikitsa Mtendere M’malo mwa Nkhondo 22
Dziŵani chifukwa chimene mmisiri wina anasiyira ntchito yake.