Zamkatimu
July 8, 2003
Kodi Chiwawa Choopsa Chingadzathetsedwe?
Ana a sukulu asanu ndi atatu ataphedwa mu Ikeda ku Japan, wina amene anapulumuka analira pamaliro awo. Ziwawa zoopsa zikuchitika padziko lonse. Kodi anthu amachitiranji zinthu zoopsa chonchi? Kodi padzapezeka njira yozithetsera?
3 Chiwawa Choopsa Chikungoipiraipira Chifukwa Chiyani?
5 Kodi Ziwawazi Zachulukiranji Chonchi?
10 Kodi Njira Yeniyeni Yothetsera Vutoli Ingapezekedi?
19 Kodi Nkhalango Zachilengedwe za M’madera Otentha Zingatheke Kutetezedwa?
21 Kodi M’nkhalangozi Tingadulemo Mitengo Mosawononga?
26 Kodi Nkhalangozi Angaziteteze Ndani?
Kodi Ndizitani Tsoka Likandigwera? 16
Masoka adzidzidzi angapangitse ana kumadzifunsa mafunso ena ovuta kwambiri. Onani malangizo osavuta komanso olimbikitsa opezera mayankho ena ofunika kwambiri.
Mmene Ndinaphera Ludzu la Mawu a Mulungu 28
Taŵerengani za sisitere amene sankakhutira ndi za Mulungu mpaka pamene anayamba kuphunzira choonadi cha m’Baibulo chomwe chinasintha moyo wake.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
AFP PHOTO/Toshifumi Kitamura