Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 10/07 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2007
  • Nkhani Yofanana
  • Maluwa Okongola Mokopa a Kuno ku Africa
    Galamukani!—2007
  • Nsomba za Shaki Zikutha
    Galamukani!—2007
  • Thandizani Ana Anu Kulimbana ndi Mavuto Awo
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Khungu la Shaki
    Kodi Zinangochitika Zokha?
Onani Zambiri
Galamukani!—2007
g 10/07 tsamba 1-2

Zamkatimu

October 2007

Tetezani Ana Anu!

Masiku ano pali anthu ambiri ogona ana motero m’pofunika kuti makolo adziwe mmene angatetezere ana awo. Nkhani ino ikuthandizani kutero.

3 Nkhani Imene Ikudetsa Nkhawa Kwambiri Makolo

4 Mmene Mungatetezere Ana Anu

9 Tetezani Ana M’Banja Lanu

12 Kodi Amwenye a ku Brazil Adzatha Onse?

16 Nsomba za Shaki Zikutha

18 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

Kodi ndizitani makolo anga akamakangana?

21 Nyumba ya Mphamvu Zamagetsi Iyamba Kuwala Mwauzimu

22 Ananeneratu za “Zipangizo Zosakazira Anthu”

27 “Sonyezani Kuti Ndinu Oyamikira”

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Linamuthandiza Kukamba Bwino Nkhani Kusukulu

Maluwa Okongola Mokopa a Kuno ku Africa 24

Anthu ambiri angadabwe kumva kuti ku Kenya kumachokera maluwa ambirimbiri kupita m’mayiko akunja. Kodi maluwawa amalimidwa bwanji?

Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira? 28

Anthu ambiri amakhulupirira bodza lakuti achibale awo amene anamwalira ali kumwamba ndipo amatha kuona abale awowo pansi pano. Kodi Baibulo limati chiyani pankhani imeneyi?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena