Zamkatimu
July 2009
Kuthandiza Anthu Ovutika Maganizo
Anthu ambiri amadwala matenda ovutika maganizo. Kodi matendawa ali ndi mankhwala?
3 Kodi Matenda Ovutika Maganizo Ndi Otani?
4 Kodi Mungathetse Bwanji Matenda Ovutika Maganizo?
6 “Mulungu wa Chitonthozo Chonse” Amathandiza
17 Albarracín Ndi Tawuni Yokongola Kwambiri
20 Mankhwala Odzikongoletsera Ochokera ku Mitengo
21 Kodi Mungakonde Kuyenda pa Galimoto Yopalasa?
Kodi Mungatani Kuti Muziyendetsa Bwino Galimoto? 11
Nkhaniyi ili ndi malangizo okuthandizani kupewa ngozi.
Kodi Kusintha Chipembedzo Chanu N’kulakwa? 28
Kodi chipembedzo chimene munabadwira n’cholondola? Bwanji ngati chitakhala chosalondola?