Zamkatimu
August 2009
N’chifukwa Chiyani Anthu Amasankhana?—Nanga Mungatani Ngati Ena Amakusankhani?
Tsiku lililonse anthu ambiri amasalidwa pazifukwa zosiyanasiyana. Kodi n’chiyani chimayambitsa tsankho? Ndipo kodi tsankho lidzatha?
3 N’chifukwa Chiyani Anthu Amasankhana?
4 Kodi Tsankho Limayamba Bwanji?
7 Chikondi Chimathetsa Tsankho
19 Kodi N’chiyani Chinayambitsa Nkhondo ya Padziko Lonse?
26 Kodi Mumatha Kusunga Zinthu Zanu Mwachinsinsi?
32 ‘Chitseko Chimene Yehova Yekha Ndi Amene Angatsegule’
Kodi Ndingatani Ngati Mayi Kapena Bambo Anga Amwalira? 10
Imfa ya mayi kapena bambo ndi yopweteka kwambiri. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene mungachite ngati mayi kapena bambo anu amwalira?
Kumwamba Kuli Zinthu Zambiri Zodabwitsa 16
Asayansi akamaphunzira zambiri zokhudza chilengedwe, m’pamenenso amazindikira kuti zimene akudziwa n’zochepa kwambiri. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu zogometsa zimene asayansi atulukira posachedwapa.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Based on NASA photo