Kodi Nkhani Yonena za Yesu Ndi Yongopeka?
Na. 5 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka ndalama zothandizira pantchito yolalikira, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.