Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira
Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com/ny.
Malemba onse m’kabuku kano achokera m’Baibulo la Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza lina. Komabe, Chichewa chake tachilemba m’kalembedwe katsopano. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures—With References.
Kosindikizidwa mu August 2017
Chichewa (we-CN)
© 1994, 2000, 2005
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania