Mlozera Nkhani
Dziwani izi: Malo amene mawu ambiri akupezeka asonyezedwa ndi mutu wa nkhani kenako ndime yake. Mwachitsanzo, mawu oyamba amene akupezeka pa mutu wakuti “Ana” ndi akuti “tchimo: 14:37.” Zimenezi zikutanthauza kuti nkhani yokhudza zoyenera kuchita ana akachita tchimo ikupezeka m’Mutu 14, ndime 37.
Akhristu omwe anasiya kulalikira: 8:26; 14:32
Akulu
amaikidwa ngati akwaniritsa zimene Malemba amanena: 4:8
kuchita zinthu mogwirizana: 5:21
kutetezera kuti mpingo ukhalebe woyera: 14:19-40
kuyesetsa kuti ukhale mkulu: 5:22
magulu ndi timagulu: 9:42-44
misonkhano: 5:37
mmene tiyenera kuwaonera: 3:14; 5:38-39
okalamba kapena odwala: 5:23-24
zimene munthu angachite kuti ayenerere: 5:4-20
Alongo
kugwira ntchito yomanga: 10:21
ngati mumpingo mulibe abale oyenera kukhala pa udindo: 6:9; 7:23
sukulu zophunzitsa Baibulo: 10:17-18
Ana
akachita tchimo: 14:37
anyamata amene akufuna kukhala pa udindo: 6:14
kupita patsogolo: 8:13-15; 10:26; tsa. 179-181
kuthandiza makolo okalamba kapena amene akudwala: 12:14
moyo wa kusukulu: 13:22-24
Anthu osauka: 12:12-15
Apainiya: 10:11-14
Apainiya apadera: 10:11, 14, 17-18
Apainiya othandiza: 10:11-12
Atumiki othandiza
kuyesetsa kuti muyenerere: 6:14
zimene munthu angachite kuti ayenerere: 6:3-6
Bungwe Lolamulira
kusonyeza kuti timalikhulupirira: 3:12-15
mmene tingalidziwire: 3:1-6
n’chifukwa chiyani tiyenera kumvera bungweli: 3:9-11; 4:9-11
Chakudya Chamadzulo cha Ambuye: 7:28-30
Chikumbutso: 7:28-30
Chitsanzo chabwino
tanthauzo lake: 6:9
Gawo
kulemba zofunikira: 9:31
la kagulu ndi la munthu pa yekha: 9:31-34
la zinenero zosiyanasiyana: 9:36-37
Gulu
mbali yakumwamba: 1:8-13
“Kapolo wokhulupirika ndi wanzeru”
kumugonjera: 15:7
kusonyeza kuti timamudalira: 3:12-15
mmene tingamudziwire: 3:4-6
Komiti
ya Dziko: 5:53
ya Utumiki ya Mpingo: 5:35
Yolankhulana ndi Achipatala: 5:40
Yoyang’anira Nyumba ya Ufumu: 11:8
Komiti ya utumiki
(Onani Komiti ya Utumiki ya Mpingo)
Komiti ya Utumiki ya Mpingo: 5:35
Kubwezeretsa: 14:34-36
Kuchita zinthu mogwirizana
chimene chimachititsa: 1:6-7; 13:28-29
kukhalabe ogwirizana: 17:20
madalitso: 4:15; 5:57; 13:30-31
motsogoleredwa ndi Khristu: 2:9-11; 4:10-11
padziko lonse: 16:6-11
Kuchotsa munthu mumpingo: 14:25-29
Kudzilekanitsa: 14:30-33
Kudzipereka ndiponso kubatizidwa
(Onani Ubatizo)
Kugonjera
(Onani Mutu)
Kuika chizindikiro anthu ochita zosalongosoka: 14:9-12
Kuikidwa kukhala mtumiki wa Mulungu: 8:3
Kulalikira uthenga wabwino
achinyamata: 8:13-15
gawo: 9:30-34
imayang’aniridwa ndi woyang’anira utumiki: 5:28
kuchitira lipoti: 8:19-29, 31-36
kugwiritsa ntchito webusaiti ya jw.org: 9:24-25
kulalikira m’magulu: 9:45-46
kulalikira mwamwayi: 9:26-29
kulimbikitsa ophunzira Baibulo kuti aziuza ena zimene akuphunzira: 8:5
kunyumba ndi nyumba: 9:3-9
kuthandiza nawo: 5:28-29, 33; 7:21; 9:7, 15, 19
kutsogolera: 5:3, 17, 29-33; 6:4
mabuku ndi magazini: 9:22-23
madera omwe anthu ake amalankhula zinenero zosiyanasiyana: 9:35-44
maonekedwe athu: 13:12
maulendo obwereza: 9:14-15
misonkhano yokonzekera utumiki wakumunda: 7:20-21
m’malo opezeka anthu ambiri: 9:11-12
m’nthawi ya atumwi: 8:1-2; 9:1, 4
ntchito yopatsidwa ndi Mulungu: 8:2
pa nthawi imene ntchito yathu ili yoletsedwa: 17:13-18
zoyenera kuchita munthu asanayambe kugwira nawo ntchitoyi: 8:6-9, 13-15
Kusamvana
kuthetsa pa nkhani zikuluzikulu: 14:13-20
kuthetsa pa nkhani zing’onozing’ono: 14:5-6
Kutumikira kumene kukufunikira ofalitsa ambiri: 10:6-9
Kuvala ndi kudzikongoletsa
amene angapatsidwe udindo: 6:9
atumiki othandiza: 6:5
kukacheza ku Beteli: 13:13
pochita zosangalatsa: 13:14
utumiki: 13:12
Kuvomereza kugwiritsa ntchito ndalama: 12:6, 9, 11
Lipoti la Mpingo Lolembapo Ntchito za Wofalitsa: 5:44; 8:10, 30
Mabuku
kufunika kwake mu utumiki: 9:22-23
kumene ndalama zimachokera: 12:2-4
kusamalira mabuku: 12:16
m’madera amene muli anthu a zinenero zosiyanasiyana: 9:36, 38
Mabungwe osiyanasiyana: 4:12
Madera amene anthu amalankhula zinenero zosiyanasiyana: 9:35-44
magulu ndi timagulu: 9:42-44
sukulu yophunzitsa chinenero: 10:10
tikakumana ndi munthu wolankhula chinenero china: 9:38-41
Makomiti Olankhulana ndi Achipatala ndiponso Magulu Oyendera Odwala: 5:40
Makomiti oweruza: 14:21-28, 34-37
Malipoti
kufunika kwake: 8:19-22, 31-36
ngati tachokapo kwakanthawi: 8:30
oyang’anira madera: 5:46, 50; 9:44
Maliro: 11:10-11
Malo a Misonkhano: 11:18-21
Maphunziro a Baibulo
kuchitira lipoti: 8:26
kulimbikitsa wophunzira kuti aziuza ena zomwe akuphunzira: 8:5
kutsogolera wophunzira ku gulu la Yehova: 9:20-21
ubwino wake: 9:16-17
Maukwati: 11:10-11
Misonkhano ya mpingo
Aisiraeli: 11:1
akulu: 5:37
ana azikhala ndi makolo awo: 11:13
cholinga: 7:1-2
kufunika kwake: 3:12; 7:4, 27; 15:7
kukambirana za malonda: 13:27
malo osonkhanako: 11:1-5, 18-19
misonkhano yachigawo: 7:25-26
misonkhano yadera: 7:24
misonkhano yokonzekera utumiki: 7:20-21; 9:45
nkhani ya onse: 7:5-10
olandira alendo: 11:14
pamene ntchito yathu ili yoletsedwa: 17:15-17
Phunziro la Baibulo la Mpingo: 7:17
Phunziro la Nsanja ya Olonda: 7:11-13
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu: 7:14-19
yochititsidwa ndi alongo: 7:23
Misonkhano yachigawo: 7:25-27
Misonkhano yadera
(Onani Msonkhano wadera)
Mpingo
(Onaninso Nyumba ya Ufumu; Misonkhano ya mpingo)
kugwirizana: 13:28-30
umatsogoleredwa ndi Yehova: 1:3; 4:4-11
watsopano ndi waung’ono: 7:22-23
Msonkhano wadera
malo: 11:18
mmene umayendetsedwera: 5:49
ndalama zoyendetsera: 12:8-11
Mutu
m’banja: 15:9-10
m’gulu la Yehova: 1:9-10; 2:5, 9-10; 15:1-2
olamulira akuluakulu: 15:11
Ndalama
za dera: 12:8-11
za ntchito ya padziko lonse: 11:15; 12:2-4
Ndandanda ya Msonkhano wa utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu 7:14-18
Nkhani ya onse: 7:5-10
Ntchito yopereka thandizo: 12:15; 16:11
Ntchito zomangamanga: 10:21-23
Gulu la Zomangamanga: 10:23
ongodzipereka kuchita utumiki wa zomangamanga: 10:23
othandiza pa ntchito ya zomangamanga m’dera lawo: 10:23
wochita utumiki wa zomangamanga: 10:23
wogwira ntchito ya zomangamanga m’dziko lina: 10:23
Ntchito: 13:25-26
Nyumba ya Ufumu
kuipereka: 11:4
kuisamalira: 11:7-8
kulipira zinthu zofunika: 11:6; 12:5-6
kumanga: 10:21-23; 11:4-5, 15-17
laibulale: 7:19
mipingo ingapo: 11:8-9
zochitika zapadera: 11:10-11
Ofalitsa
(Onani Ofalitsa a mpingo; Ofalitsa osabatizidwa)
Ofalitsa a mpingo
(Onaninso Ofalitsa osabatizidwa)
ana: 8:13-14
atsopano: 8:5-6
kusamuka: 8:30
kuti ayenerere kukhala ofalitsa: 8:8
kuwathandiza: 5:28-29, 33; 7:21; 9:7, 15, 19
okalamba ndi odwala: 8:29
Ofalitsa osabatizidwa
akachita tchimo: 14:38-40
ana: 8:13-15
kuti munthu ayenerere: 8:6-12
pomanga kapena kukonza Nyumba ya Ufumu: 11:17
Ofesi ya nthambi
mmene tingavalire ndi kudzikongoletsa popitako: 13:13
ngati zili zosatheka kulankhulana ndi ofesi ya nthambi: 17:15-17
ntchito zake: 4:13
zopereka zopita ku: 12:2-4
Oimira likulu: 5:55-56
Olandira alendo: 11:14
Oyang’anira
(Onani Akulu)
Phunziro la Nsanja ya Olonda: 7:11-13
Tchimo
(Onaninso Kudzilekanitsa; Kuchotsa munthu mumpingo; Kuika chizindikiro anthu ochita zosalongosoka; Kusamvana; Kubwezeretsa)
ana: 14:37
kulakwira Mkhristu mnzathu: 14:5-6, 13-20
ofalitsa osabatizidwa: 14:38-40
tchimo lalikulu: 14:21-33
zilengezo zokhudza: 14:24, 29, 33, 39-40
Timagulu ta utumiki wakumunda
kugawa ofalitsa m’timagulu: 5:35
kusamalira Nyumba ya Ufumu: 11:7
misonkhano yokonzekera utumiki wakumunda: 7:20-21
oyang’anira: 5:29-34
udindo wa atumiki othandiza: 6:12
Ubatizo
ana: tsa. 179-181
kuikidwa kukhala mtumiki wa Mulungu: 8:3
mafunso a ubatizo: tsa. 185-207
ofalitsa osabatizidwa: tsa. 182-184
pa misonkhano yadera, yachigawo: 7:24, 26
tanthauzo lake: 8:16-18
Ukhondo
makhalidwe: 13:6-7
Nyumba ya Ufumu: 11:7-8
ukhondo: 13:8-12
Utumiki wa pa Beteli: 10:19-20
Webusaiti ya JW.ORG: 9:24-25
Wogwirizanitsa ntchito za akulu
kuchezera kwa woyang’anira dera: 5:42-44
kuwerengera maakaunti: 12:7
Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu: 7:18
ntchito zake: 5:26
ofuna kubatizidwa: 8:18; tsa. 208-212
Woyang’anira dera
amapempha zokhazikitsa mpingo: 7:22
kuchezera kwake: 5:41-48
kulankhula naye mukafuna kuwonjezera utumiki: 10:6, 10, 16, 20
kumuchereza: 5:50
magulu: 9:44
Woyang’anira utumiki: 5:28, 32; 9:31, 37, 45
Yehova Mulungu
kukhala naye pa ubwenzi: 17:1-3
Wolamulira wa Chilengedwe Chonse: 15:1-4
Yesu Khristu
kugonjera Yehova: 15:5
Mkulu wa Ansembe: 2:4
Mpulumutsi: 2:3
Zilengezo
kubwezeretsa: 14:36
kudzilekanitsa: 14:33
kudzudzula: 14:24
ofalitsa osabatizidwa: 8:12; 14:39-40
za wochotsedwa: 14:29
zopereka: 12:6
Zochitika za kusukulu: 13:22-24
Zolinga
kuphunzira chinenero china: 10:10
kutumikira kumene kukufunika ofalitsa ambiri: 10:6-9
kutumikira pa Beteli: 10:19-20
kuyang’anira dera: 10:16
ntchito yomanga: 10:21-23
ofalitsa: 10:4-5
sukulu zophunzitsa Baibulo: 10:17-18
ubwino wokhala nazo: 10:24-26
umishonale: 10:15
upainiya: 10:11-14
zotheka kuzikwaniritsa: 8:37
Zopereka: 3:13; 11:6-7, 15; 12:2-11
Zosangalatsa: 13:15-21