Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 44
  • Pemphero la Munthu Wovutika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pemphero la Munthu Wovutika
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Pemphero la Munthu Wovutika
    Imbirani Yehova
  • Mulungu Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova
  • Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Ndithandizeni Ndikhale Wolimba Mtima
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 44

NYIMBO 44

Pemphero la Munthu Wovutika

Losindikizidwa

(Salimo 4:1)

  1. 1. M’lungu ndikupempha:

    “Imvani pemphero langa.”

    Zilonda zanga zakula

    sizikupolanso.

    Kuvutika ndi

    maganizo kwandifoola,

    Ndichitireni chifundo

    M’lungu wotonthoza.

    (KOLASI)

    Ndidzutseni ndipirire.

    Nkhawa zanga zichotseni.

    Pamavuto n’thandizeni.

    Yehova ndilimbitseni.

  2. 2. N’kafooka mawu anu

    amanditonthoza.

    Amafotokoza mfundo

    zondigwira mtima.

    Ndidziwe kuti chikondi

    chanu n’chachikulu,

    Ndikumbukire kuti n’choposa

    mtima wanga.

    (KOLASI)

    Ndidzutseni ndipirire.

    Nkhawa zanga zichotseni.

    Pamavuto n’thandizeni.

    Yehova ndilimbitseni.

(Onaninso Sal. 42:6; 119:28; Aroma 8:​26; 2 Akor. 4:16; 1 Yoh. 3:20.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena