Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • rr tsamba 5
  • Matanthauzo a Zinthu Zina Zapadera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Matanthauzo a Zinthu Zina Zapadera
  • Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
rr tsamba 5

Matanthauzo a Zinthu Zina Zapadera

MABOKOSI

Bokosi limene likusonyeza nambala ya mutu komanso chilembo cha afabeti.

Mabokosi amene ali m’buku lino ali ndi nambala ya mutu komanso chilembo cha afabeti. Mwachitsanzo mabokosi atatu amene ali m’Mutu 10 apatsidwa manambala awa: 10A, 10B ndi 10C. M’buku la pachipangizo chamakono, munthu angathe kuona mabokosi onse nthawi imodzi m’gawo lakuti “Mabokosi.” Buku la pachipangizo chamakono lili ndi zinthu zina zimene m’buku losindikiza mulibe.

MATCHATI

Mabokosi ambiri ali ndi matchati amene akusonyeza nthawi imene zinthu zinazake zinachitika. Pamene mizere yapindika ngati mmene tikuonera pachitsanzochi, zikusonyeza kuti sanaike nthawi yonse imene inadutsa n’cholinga choti mzere ukwanire pachinthunzichi. (Mwachitsanzo, onani bokosi 8B.) Nthawi zina mizere yopindikayi imaimira nthawi imene sikudziwika kutalika kwake.​—Onani bokosi 9E.

Tchati chimene chikusonyeza nthawi pakati pa 607 B.C.E. ndi 1914 C.E.

Mawu achidule amene agwiritsidwa ntchito m’bukuli:

  • B.C.E.​—Nyengo yathu ino isanafike

  • C.E.​—Nyengo yathu ino

  • c.​—cha m’ma

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena