Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Yambani Kuphunzira Baibulo
Photo Credit: Page 13, Babylon’s ruins: Image © Homo Cosmicos/Shutterstock
Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Malifalensi onse amene ali m’kabukuka ndi ofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova.
Kosindikizidwa mu January 2021
Chichewa (lffi-CN)
© 2021
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA