Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Muzikonda Anthu—Muziwaphunzitsa
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’kabukuka achokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kosindikizidwa mu May 2023
Chichewa (lmd-CN)
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania