Mutu wa Bukuli/Tsamba la Ofalitsa
Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2025
Lemba la Chaka “Mʼpatseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.”—Salimo 96:8.
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kosindikizidwa mu June 2024
Chichewa (es25-CN)
© 2024
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA