Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w04 3/15 tsamba 32
  • Tsiku Lofunika Kulikumbukira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tsiku Lofunika Kulikumbukira
  • Nsanja ya Olonda—2004
Nsanja ya Olonda—2004
w04 3/15 tsamba 32

Tsiku Lofunika Kulikumbukira

MADZULO oti aphedwa maŵa, Yesu Kristu anapatsa atumwi ake mkate wopanda chotupitsa ndi chikho cha vinyo wofiira ndi kuwauza kuti adye ndi kumwa. Anawauzanso kuti: “Chitani ichi chikumbukiro changa.”​—Luka 22:19.

Chaka chino tsiku lokumbukira mwambo umenewu ndi Lamlungu, pa April 4, dzuŵa litaloŵa. Mboni za Yehova padziko lonse zidzasonkhana usiku umenewu kuti zichite mwambo wa Chikumbutsowu. Zidzachita mwambo umenewu mmene Yesu analamulirira. Mukuitanidwa kuti mudzakhale nawo. Chonde funsani Mboni za Yehova kwanuko kuti zikuuzeni nthaŵi ndiponso malo enieni a msonkhano wapadera umenewu.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena