Tsamba 32
◼ Anthu akamapemphera kuti Ufumu wa Mulungu ubwere, kodi kwenikweni amakhala akupempha chiyani?
◼ Kodi mungatani kuti muphunzire kuganiza kaye musanalankhule?
◼ Kodi Mulungu anachititsa kuti anthu akhaleko mwa kuwasintha kuchokera ku zinthu zina?
◼ Kodi Eliya anali ndani, ndipo tingaphunzire chiyani kwa iye?
◼ Kodi tingatsimikize bwanji kuti maulosi a m’Baibulo sanalembedwe zinthu zomwe analoserazo zitachitika kale?
◼ N’chifukwa chiyani Yehova Mulungu ali Atate wabwino kwambiri kuposa wina aliyense?
◼ Kodi ndi zoona kuti anthu okhulupirira nyenyezi anabwera ndi mphatso kwa Yesu usiku umene iye anabadwa?