Tsamba 32
◼ Kodi Baibulo linalosera kale mavuto a masiku anowa? Onani tsamba 6.
◼ Kodi n’zotheka kuti anthufe titsanzire Mulungu? Ngati n’zotheka, kodi tingam’tsanzire motani? Onani tsamba 15.
◼ Kodi bambo amafunika kuti aziwachitira zotani ana ake? Onani tsamba 18.
◼ Kodi tingaphunzire chiyani kwa Mariya poona zimene zinachitika panthawi ya kubadwa kwa Yesu? Onani tsamba 22.
◼ Ngati Adamu anali munthu wangwiro kodi zinatheka bwanji kuti achimwe? Onani tsamba 27.