Tsamba 32
◼ Kodi pali umboni wotani wosonyeza kuti Yesu anakhalapodi? Onani tsamba 7.
◼ N’chifukwa chiyani muyenera kupeza umboni womwe ungakuthandizeni kukhulupirira kuti Mulungu alipodi? Onani tsamba 9.
◼ Kodi mungatani kuti muthandize mwana wanu wachinyamata kuti akule bwino? Onani masamba 10 mpaka 12.
◼ Kodi mizimu yoipa ndi yoopsa motani? Onani tsamba 20.
◼ Kodi masiku ano Mulungu amapatsa anthu mphamvu zochiritsa mozizwitsa? Onani tsamba 28.