Tsamba 32
◼ Ngati muli wokhulupirika kwa Mulungu, kodi iye adzakudalitsani pokupatsani chuma? Onani tsamba 4.
◼ Kodi ndalama n’zimene zimapangitsa munthu kukhala wosangalaladi? Onani tsamba 9.
◼ Kodi pangakhale vuto ngati simukhulupirira kuti Adamu ndi Hava anali anthu enieni? Onani tsamba 12.
◼ Kodi mukuganiza kuti kubwezera n’kwabwino kapena n’koipa? Onani tsamba 20.
◼ Kodi mungapeze chiyani m’nyanja yaikulu ya ku Central America? Onani tsamba 25.