Tsamba 32
◼ Kodi anthu onse abwino amapitadi kumwamba? Onani tsamba 6.
◼ Kodi Mariya analidi “Amayi a Mulungu”? Onani tsamba 8.
◼ Kodi Mulungu amasangalala anthu akamagwiritsa ntchito zithunzi ndi mafano pomulambira? Onani tsamba 9.
◼ N’chiyani chingakuthandizeni ngati mkazi kapena mwamuna wanu ali ndi matenda aakulu kapena anavulala kwambiri? Onani tsamba 10 mpaka 12.
◼ Kodi uthenga wa m’Baibulo unasinthidwa? Onani tsamba 13 ndi 14.
◼ Kodi aliyense m’banja angatani kuti banjalo lizisangalala? Onani tsamba 16 ndi 17.