Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w09 12/1 tsamba 32
  • Tsamba 32

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tsamba 32
  • Nsanja ya Olonda—2009
Nsanja ya Olonda—2009
w09 12/1 tsamba 32

Tsamba 32

◼ Dziwani njira yabwino kwambiri yothetsera mavuto onse amene tikukumana nawo masiku ano. Onani tsamba 5.

◼ Anthu amene anapulumuka pamene mwana wasukulu anapha anthu pasukulu ina ku Winnenden, m’dziko la Germany, akufotokoza chimene chikuwathandiza kupirira zoopsazi. Onani tsamba 9.

◼ Kodi ndi Mfumu Herode uti amene ankafuna kupha Yesu ali wakhanda? Onani tsamba 13.

◼ Kodi mukudziwapo chiyani pachikondwerero chimene chimachitika ku Asia pakapita mwezi umodzi m’chaka chatsopano? Onani tsamba 20.

◼ Dziwani nkhani yokhudza nyimbo za m’nthawi ya Baibulo, pophunzira moyo wa Mfumu Davide. Onani tsamba 26.

◼ Panthawi imene Yesu anali modyeramo ziweto, kodi panabweradi mafumu atatu, kapena kuti anzeru a kum’mawa, kudzalambira? Onani tsamba 31.

[Mawu a Chithunzi patsamba 32]

Starving children: WHO/​OXFAM

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena