Zamkatimu
April 1, 2010
Magazini Yapadera
Munthu Amene Anasintha Dziko—Kodi Uthenga Wake Umakukhudzani Bwanji?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Munthu Amene Anasintha Dziko
4 Uthenga wa Yesu Khristu Ndi Wamphamvu Kwambiri
5 Kodi Yesu Anati Iye Ndi Ndani?
6 Kodi Yesu Anaphunzitsa Chiyani za Mulungu?
8 Kodi Yesu Anaphunzitsa Chiyani za Ufumu wa Mulungu?
11 Kodi Uthenga wa Yesu Khristu Umakukhudzani Bwanji?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
20 Yandikirani Mulungu —“Mpando Wachifumu Wako Udzakhazikika”
21 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo —Mbuye Wake Anam’phunzitsa Kukhululukira Ena
30 Phunzitsani Ana Anu—Yesu Anaphunzira Kumvera
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
16 Sunagoge —Anali Malo Amene Yesu ndi Ophunzira Ake Ankakonda Kulalikira
26 Kodi Baibulo Limafotokoza Zonse Zokhudza Yesu?