Zamkatimu
July 1, 2010
Kodi Dzina la Mulungu Mumalidziwa?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi N’zotheka Kulidziwa Dzina la Mulungu?
4 Kodi Kudziwa Dzina la Mulungu Kumatanthauza Chiyani?
5 Zimene Zikuchititsa Kuti Anthu Asalidziwe Dzina la Mulungu
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
14 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo —Anauza Mulungu Zakukhosi Kwake
28 Zimene Owerenga Amafunsa . . .
29 Yandikirani Mulungu—Amaona Zabwino mwa Anthu
30 Zoti Achinyamata Achite—Zimene Mungachite Kuti Mupeze Anzanu Enieni
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
10Zimene Mungachite Kuti Muthandize Mnzanu Amene Akudwala
19 Mfundo 7 Zimene Zingakuthandizeni Kuti Mupindule ndi Kuwerenga Baibulo
22 Kodi N’chifukwa Chiyani Yesu Sankalowerera Ndale?
26 Wosindikiza Mabuku Amene Anathandiza Kufalitsa Baibulo