Zamkatimu
November 1, 2010
Mfundo Zisanu Zothandiza Kuti Muzikhutira ndi Zimene Muli Nazo
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi Munthu Angakhaledi Wokhutira ndi Zimene ali Nazo?
4 MFUNDO YOYAMBA. Muzikonda Anthu, Osati Ndalama Kapena Katundu
5 MFUNDO YACHIWIRI. Pewani Kudziyerekezera ndi Ena
6 MFUNDO YACHITATU. Khalani Ndi Mtima Woyamikira
7 MFUNDO YACHINAYI. Muzisankha Mwanzeru Anthu Ocheza Nawo
8 MFUNDO YACHISANU. Pezani Zosowa Zanu Zauzimu
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
12 Chinsinsi cha Banja Losangalala—Muzikambirana ndi Ana Anu Nkhani Zokhudza Kugonana
16 Zimene Tikuphunzira kwa Yesu—Mmene Angelo Amakhudzira Moyo Wathu
25 Yandikirani Mulungu—“Adzalola Kuti Um’peze”
26 Chinthu Chapadera Kwambiri M’mbiri Yathu Yauzimu
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
9 Muzitonthoza Anthu Amene Aferedwa, Ngati Mmene Yesu Anachitira
22 Moyo wa Akhristu Oyambirira—Maulendo Okafika Kumalekezero a Dziko Lapansi