Zamkatimu
April 1, 2011
Yesu—Kodi Anachokera Kuti? Anachita Zotani pa Moyo Wake? N’chifukwa Chiyani Anafa?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi Yesu Khristu Ndani Kwenikweni?
6 Yesu—Kodi Anachita Zotani pa Moyo Wake?
8 Yesu—N’chifukwa Chiyani Anafa?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
11 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—“Ndimakhulupirira”
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Mulungu Analengeranji Dziko Lapansili?
23 Yandikirani Mulungu—Okalamba Adzakhalanso Achinyamata
24 Phunzitsani Ana Anu—Kodi Nthawi Zina Umaona Kuti Uli Wekha Ndiponso Umachita Mantha?
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
18 Mlandu Umene Unaweruzidwa Mopanda Chilungamo Kuposa Milandu Yonse