Zamkatimu
September 1, 2011
Kodi Amene Akulamulira Dzikoli Ndani Kwenikweni?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi Pali Winawake Amene Amachititsa Zoipa Zonsezi?
4 Kodi Amene Akulamulira Dzikoli Ndani Kwenikweni?
7 Baibulo Limatiuza Wolamulira wa Dzikoli
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
10 Zimene Owerenga Amafunsa . . .
15 Yandikirani Mulungu—“Inu Yehova, . . . Mukundidziwa”
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Mungatani Kuti Muyandikire Mulungu?
24 Kalata Yochokera ku Congo (Kinshasa)
30 Zoti Achinyamata Achite—Anamunamizira Mlandu
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
11 “Mitundu 7 ya Mbewu” za M’dziko Labwino
18 Olivétan—‘Mnyamata Wosatchuka Amene Anamasulira’ Baibulo M’Chifulenchi
21 Kodi Muyenera Kukhoma Misonkho?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Photo: Alain Leprince - La Piscine-musée, Roubaix /Courtesy of the former Bouchard Museum, Paris