Zamkatimu
May 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino ndi wathu.
Kodi Chipembedzo ndi Ndale Ziyenera Kuyendera Limodzi?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi Yesu Angayankhe Bwanji Funso Limeneli?
5 Kodi Yesu Ankachita Nawo Ndale?
6 Kodi Akhristu Ayenera Kulowerera Ndale?
8 Kodi Zimene Akhristu Amaphunzitsa Zimathandiza Bwanji Anthu a M’dera Lawo?
10 Kodi Tingakhale Bwanji Mkhristu Weniweni Komanso Nzika Yodalirika?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
12 Chinsinsi cha Banja Losangalala—Zimene Mungachite Kuti Muyambirenso Kukhulupirirana
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi N’chiyani Chidzachitikire Zipembedzo?
22 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Akhristu a M’nthawi ya Atumwi Ankachita Nawo Ndale?
24 Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo
31 Yandikirani Mulungu—Amapereka Mphoto kwa Onse Omwe Amamutumikira
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI: