Zamkatimu
September 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Kodi Mulungu Amaona Kuti Akazi Ndi Otsika?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Mavuto Amene Akazi Amakumana Nawo
4 Kodi Mulungu Amaona Kuti Akazi Ndi Otsika?
8 Mulungu Amafuna Kuti Akazi Azilemekezedwa
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi pa Tsiku la Chiweruzo Padzachitika Zotani?
21 Yandikirani Mulungu—‘Mitundu Idzadziwa Kuti Ine Ndine Yehova’
23 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi akazi a Mboni za Yehova Amaphunzitsa Mawu a Mulungu?
30 Phunzitsani Ana Anu—Gehazi Anapeza Mavuto Chifukwa cha Dyera
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
12 Tsopano Ndikudziwa Mulungu Amene Ndikum’tumikira