Zamkatimu
November 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Kodi Mungakonde Kum’funsa Chiyani Mulungu?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi N’koyenera Kumufunsa Mulungu Mafunso?
4 Funso Loyamba: Kodi Cholinga cha Moyo Wanga N’chiyani?
6 Funso Lachiwiri: Kodi Chidzandichitikire N’chiyani Ndikadzamwalira?
8 Funso Lachitatu: N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Ndizivutika?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
18 Chinsinsi cha Banja Losangalala—Zimene Mungachite Ngati Muli Ndi Ngongole
22 Yandikirani Mulungu—‘Kodi Yehova Akufuna Chiyani kwa Ife?’
23 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Kukhala Ndi Chikhulupiriro N’kusaganiza Bwino?
24 Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
29 Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Ulaya Linagamula Kuti Munthu Ali Ndi Ufulu Wokana Kulowa Usilikali