Zamkatimu
July 1, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
NKHANI YA PACHIKUTO
KODI PALI CHIPEMBEDZO CHOMWE TINGACHIKHULUPIRIRE?
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kufufuza za Chipembedzo Chanu? 3
Kodi Zipembedzo Mungazikhulupirire pa Nkhani ya Ndalama? 4
Kodi Zipembedzo Mungazikhulupirire pa Nkhani ya Nkhondo? 5
Kodi Zipembedzo Mungazikhulupirire pa Nkhani ya Makhalidwe Abwino? 6
Kodi Pali Chipembedzo Chimene Mungachikhulupirire? 7
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
Chinsinsi cha Banja Losangalala—Mmene Mungakhalire Osangalala Ngati Mwakwatira Kapena Kukwatiwanso 8
Yandikirani Mulungu—‘Amadzaza Mitima Yathu’ 11
Kucheza ndi Munthu Wina—Kodi Mulungu Amamva Chisoni Tikamavutika? 14
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA | www.jw.org
MAFUNSO AMENE ANTHU AMAKONDA KUFUNSA KAWIRIKAWIRI OKHUDZA MBONI ZA YEHOVA—N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Anthu Amene Ali Kale ndi Chipembedzo Chawo?
(Fufuzani pa mawu akuti NKHANI ZOKHUDZA MBONI ZA YEHOVA > MAFUNSO AMENE ANTHU AMAFUNSA KAWIRIKAWIRI)