Zamkatimu
September 1, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI YA PACHIKUTO
N’chifukwa Chiyani Anthu Akuvutika Chonchi? Nanga Mavuto Amenewa Adzatha Liti?
Anthu Ambiri Osalakwa Akuphedwa 3
N’chifukwa Chiyani Anthu Akukumana ndi Mavuto Onsewa? 4
Mavuto Onsewa Atha Posachedwapa 6
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
Ndife Osauka Koma Olemera Mwauzimu 8
Kodi Zinenero Zathu Zinayambira pa “Nsanja ya Babele”? 10
Yandikirani Mulungu—“Mulungu Amakonda Munthu Wopereka Mokondwera” 13
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo 16
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA | www.jw.org
MAFUNSO AMENE ANTHU AMAKONDA KUFUNSA KAWIRIKAWIRI OKHUDZA MBONI ZA YEHOVA—Kodi Ndalama Zoyendetsera Ntchito Yanu Zimachokera Kuti?
(Fufuzani pa mawu akuti NKHANI ZOKHUDZA MBONI ZA YEHOVA > MAFUNSO AMENE ANTHU AMAFUNSA KAWIRIKAWIRI)