Zamkatimu
November 1, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI YA PACHIKUTO
Mabodza Omwe Amalepheretsa Anthu Kukonda Mulungu
TSAMBA 3 MPAKA 7
Zimene Zimalepheretsa Ena Kukonda Mulungu 3
Bodza Loyamba: Mulungu Alibe Dzina 4
Bodza Lachiwiri: Mulungu ndi Wosamvetsetseka 5
Bodza Lachitatu: Mulungu ndi Wankhanza 6
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
Chinsinsi cha Banja Losangalala—Kodi Mungatani Kuti Musamakangane ndi Mwana Wanu? 8
Yandikirani Mulungu—“Amapereka Mphoto kwa Anthu Omufunafuna Ndi Mtima Wonse” 11
Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—‘Anaonedwa Ngati Wolungama Chifukwa cha Ntchito Zake’ 12
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo 16
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA | www.pr2711.com
MAFUNSO OKHUDZA MBONI ZA YEHOVA AMENE ANTHU AMAFUNSA KAWIRIKAWIRI—Kodi Mumakhulupirira Kuti Chipembedzo Cholondola N’chanu Chokha?
(Fufuzani pa mawu akuti ZOKHUDZA IFEYO > MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI)