Zamkatimu
December 1, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Mulungu Akhoza Kukhala Mnzanu Wapamtima
TSAMBA 3 MPAKA 7
Kodi N’zotheka Mulungu Kukhala Mnzanu Wapamtima? 3
Kodi Mumadziwa Ndiponso Kutchula Dzina la Mulungu? 4
Kodi Mumalankhulana ndi Mulungu? 5
Kodi Mumachita Zomwe Mulungu Amafuna? 6
Palibe Chinthu Chabwino Kwambiri Kuposa Kukhala pa Ubwenzi Ndi Mulungu 7
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
Kodi Mumzinda wa Timgad Munkachitika Zotani? 8
Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Ndi Zinthu Ziti Zomwe Tiyenera Kudziwa pa Nkhani ya Khirisimasi? 11
“Kuzindikira Kumachititsa Munthu Kubweza Mkwiyo” 12
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo 16
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU YA | www.pr2711.com/ny
MUNGAPEZE YANKHO LA M’BAIBULO LA FUNSO ILI—Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Yosaoneka?
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)